Yesaya 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yangʼanani kwa atate anu Abulahamu,Ndi kwa Sara+ amene anakuberekani.* Chifukwa Abulahamu anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+Koma ndinamudalitsa ndi kuchulukitsa mbadwa zake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:2 Yesaya 2, ptsa. 166-168
2 Yangʼanani kwa atate anu Abulahamu,Ndi kwa Sara+ amene anakuberekani.* Chifukwa Abulahamu anali munthu mmodzi pamene ndinamuitana,+Koma ndinamudalitsa ndi kuchulukitsa mbadwa zake.+