Yesaya 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chilungamo changa chayandikira.+ Chipulumutso changa chikubwera kwa iwe+Ndipo manja anga adzaweruza mitundu ya anthu.+ Zilumba zidzayembekezera ine+Ndipo zidzadikira dzanja langa.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:5 Yesaya 2, ptsa. 169-170
5 Chilungamo changa chayandikira.+ Chipulumutso changa chikubwera kwa iwe+Ndipo manja anga adzaweruza mitundu ya anthu.+ Zilumba zidzayembekezera ine+Ndipo zidzadikira dzanja langa.*