Yesaya 51:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa njenjete* idzawadya ngati chovalaNdipo kachilombo kodya zovala kadzawadya* ngati thonje.+ Koma chilungamo changa chidzakhala mpaka kalekaleNdipo chipulumutso changa chidzafikira mibadwo yonse.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:8 Yesaya 2, ptsa. 171-172
8 Chifukwa njenjete* idzawadya ngati chovalaNdipo kachilombo kodya zovala kadzawadya* ngati thonje.+ Koma chilungamo changa chidzakhala mpaka kalekaleNdipo chipulumutso changa chidzafikira mibadwo yonse.”+