Yesaya 51:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:10 Yesaya 2, ptsa. 172-173
10 Kodi si iwe amene unaumitsa nyanja, amene unaumitsa madzi akuya kwambiri?+ Si iwe kodi amene unapangitsa kuti pansi pa nyanja pakhale njira yoti anthu owomboledwa awolokerepo?+