Yesaya 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ine ndine Yehova Mulungu wako,Amene ndimavundula nyanja nʼkupangitsa kuti mafunde ake achite phokoso+Dzina langa ndine Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:15 Yesaya 2, tsa. 175
15 Koma ine ndine Yehova Mulungu wako,Amene ndimavundula nyanja nʼkupangitsa kuti mafunde ake achite phokoso+Dzina langa ndine Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.+