Yesaya 51:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ana ako akomoka.+ Agona pamphambano za misewu yonseNgati nkhosa zamʼtchire zimene zakodwa mu ukonde. Iwo akhuta mkwiyo wa Yehova, akhuta kudzudzula kwa Mulungu wako.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 51:20 Yesaya 2, ptsa. 176-179
20 Ana ako akomoka.+ Agona pamphambano za misewu yonseNgati nkhosa zamʼtchire zimene zakodwa mu ukonde. Iwo akhuta mkwiyo wa Yehova, akhuta kudzudzula kwa Mulungu wako.”