Yesaya 52:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwe Yerusalemu dzuka, sansa fumbi ndipo ukhale pampando. Masula zingwe zimene zili mʼkhosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni* amene unagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:2 Yesaya 2, ptsa. 180-182
2 Iwe Yerusalemu dzuka, sansa fumbi ndipo ukhale pampando. Masula zingwe zimene zili mʼkhosi mwako, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni* amene unagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina.+