Yesaya 52:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita kukakhala ku Iguputo ngati alendo.+Kenako Asuri anawapondereza popanda chifukwa. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:4 Yesaya 2, ptsa. 182-183
4 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita kukakhala ku Iguputo ngati alendo.+Kenako Asuri anawapondereza popanda chifukwa.