Yesaya 52:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Pa chifukwa chimenecho anthu anga adzadziwa dzina langa.+Pa chifukwa chimenecho adzadziwa pa tsiku limenelo kuti ineyo ndi amene ndikulankhula. Ndithu ndi ineyo.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:6 Yesaya 2, ptsa. 183-185
6 “Pa chifukwa chimenecho anthu anga adzadziwa dzina langa.+Pa chifukwa chimenecho adzadziwa pa tsiku limenelo kuti ineyo ndi amene ndikulankhula. Ndithu ndi ineyo.”