Yesaya 52:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mabwinja a mu Yerusalemu+ sangalalani, nonse pamodzi mufuule mosangalala,Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo wawombola Yerusalemu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:9 Yesaya 2, ptsa. 190-191 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 12
9 Inu mabwinja a mu Yerusalemu+ sangalalani, nonse pamodzi mufuule mosangalala,Chifukwa Yehova watonthoza anthu ake+ ndipo wawombola Yerusalemu.+