Yesaya 52:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mofanana ndi zimenezi iye adzadabwitsa mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu akadzamuona adzatseka pakamwa pawo,*+Chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo,Ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 52:15 Yesaya 2, tsa. 197 Galamukani!,12/8/1998, tsa. 29
15 Mofanana ndi zimenezi iye adzadabwitsa mitundu yambiri ya anthu.+ Mafumu akadzamuona adzatseka pakamwa pawo,*+Chifukwa iwo adzaona zimene sanauzidwepo,Ndipo adzaganizira zimene sanamvepo.+