Yesaya 53:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pawinawake* ndiponso ngati muzu wotuluka mʼnthaka youma. Saoneka ngati munthu wapadera kapena waulemerero,+Ndipo tikamuona, maonekedwe ake si ochititsa chidwi moti ife nʼkukopeka naye.* Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 53:2 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Yesaya 2, ptsa. 199-200
2 Iye adzaphuka ngati nthambi+ pamaso pawinawake* ndiponso ngati muzu wotuluka mʼnthaka youma. Saoneka ngati munthu wapadera kapena waulemerero,+Ndipo tikamuona, maonekedwe ake si ochititsa chidwi moti ife nʼkukopeka naye.*