Yesaya 53:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.Ndi ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mʼbadwo wa makolo ake?* Popeza iye anadulidwa mʼdziko la anthu amoyo.+Iye anakwapulidwa* chifukwa cha zolakwa za anthu anga.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 53:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2021, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 147/15/1996, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 205-208
8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.Ndi ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mʼbadwo wa makolo ake?* Popeza iye anadulidwa mʼdziko la anthu amoyo.+Iye anakwapulidwa* chifukwa cha zolakwa za anthu anga.+
53:8 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),5/2021, tsa. 3 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 147/15/1996, tsa. 8 Yesaya 2, ptsa. 205-208