Yesaya 54:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kulitsa tenti yako.+ Tambasula nsalu za chihema chako chachikulu. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za tenti yakoNdipo ulimbitse zikhomo zake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:2 Yesaya 2, ptsa. 221-222 Nsanja ya Olonda,1/1/1995, tsa. 16
2 “Kulitsa tenti yako.+ Tambasula nsalu za chihema chako chachikulu. Usaumire pochita zimenezi. Talikitsa zingwe za tenti yakoNdipo ulimbitse zikhomo zake.+