Yesaya 54:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Usachite mantha,+ chifukwa sudzachititsidwa manyazi.+Usachite manyazi, chifukwa sudzakhumudwitsidwa. Iwe udzaiwala manyazi apaubwana wako,Ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:4 Yesaya 2, ptsa. 221, 223-224
4 Usachite mantha,+ chifukwa sudzachititsidwa manyazi.+Usachite manyazi, chifukwa sudzakhumudwitsidwa. Iwe udzaiwala manyazi apaubwana wako,Ndipo sudzakumbukiranso kunyozeka kwa paumasiye wako.