Yesaya 54:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova anakuitana ngati kuti unali mkazi wosiyidwa komanso amene ali ndi chisoni,*+Ngati mkazi amene anakwatiwa ali mtsikana kenako nʼkusiyidwa,” akutero Mulungu wako. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:6 Yesaya 2, tsa. 224
6 Yehova anakuitana ngati kuti unali mkazi wosiyidwa komanso amene ali ndi chisoni,*+Ngati mkazi amene anakwatiwa ali mtsikana kenako nʼkusiyidwa,” akutero Mulungu wako.