Yesaya 54:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi amʼnthawi ya Nowa sadzamizanso dziko lapansi,+Ndikulumbiranso kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:9 Yesaya 2, ptsa. 226-227
9 “Kwa ine, zimenezi zili ngati masiku a Nowa.+ Monga mmene ndinalumbirira kuti madzi amʼnthawi ya Nowa sadzamizanso dziko lapansi,+Ndikulumbiranso kuti sindidzakukwiyira kapena kukudzudzula.+