Yesaya 54:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mapiri akhoza kuchotsedwa,Ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,Koma chikondi changa chokhulupirika sichidzachotsedwa pa iwe,+Ndipo pangano langa lamtendere silidzagwedezeka,”+ akutero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:10 Yesaya 2, ptsa. 226-227
10 Mapiri akhoza kuchotsedwa,Ndipo zitunda zikhoza kugwedezeka,Koma chikondi changa chokhulupirika sichidzachotsedwa pa iwe,+Ndipo pangano langa lamtendere silidzagwedezeka,”+ akutero Yehova, amene akukuchitira chifundo.+