Yesaya 54:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Iwe mkazi amene uli pamavuto,+ amene ukukankhidwa ndi mphepo yamkuntho ndiponso amene sunatonthozedwe,+Ine ndikukumanga ndi miyala komanso simenti yolimba,Ndipo ndikumanga maziko ako ndi miyala ya safiro.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:11 Yesaya 2, ptsa. 227-228
11 “Iwe mkazi amene uli pamavuto,+ amene ukukankhidwa ndi mphepo yamkuntho ndiponso amene sunatonthozedwe,+Ine ndikukumanga ndi miyala komanso simenti yolimba,Ndipo ndikumanga maziko ako ndi miyala ya safiro.+