Yesaya 54:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati aliyense atakuukira,Sadzakhala kuti watumidwa ndi ine. Aliyense amene adzakuukire adzagwa chifukwa cha iwe.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:15 Yesaya 2, ptsa. 227, 229
15 Ngati aliyense atakuukira,Sadzakhala kuti watumidwa ndi ine. Aliyense amene adzakuukire adzagwa chifukwa cha iwe.+