Yesaya 54:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndi amene ndinalenga mmisiri,Amene amauzira moto wamakalaNʼkupanga chida chankhondo ndi luso lake. Ine ndinalenganso munthu wowononga kuti aziwononga.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 54:16 Yesaya 2, ptsa. 229-230
16 Ine ndi amene ndinalenga mmisiri,Amene amauzira moto wamakalaNʼkupanga chida chankhondo ndi luso lake. Ine ndinalenganso munthu wowononga kuti aziwononga.+