Yesaya 55:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mofanana ndi mvula komanso sinowo* zimene zimagwa kuchokera kumwambaNdipo sizibwerera kumeneko mpaka zitanyowetsa kwambiri nthaka nʼkuchititsa kuti mbewu zimere ndi kubereka zipatso,Nʼkupereka mbewu kuti anthu adzale komanso chakudya kuti adye, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:10 Nsanja ya Olonda,9/1/2008, tsa. 27 Galamukani!,12/2008, ptsa. 6-7 Yesaya 2, ptsa. 244-246
10 Mofanana ndi mvula komanso sinowo* zimene zimagwa kuchokera kumwambaNdipo sizibwerera kumeneko mpaka zitanyowetsa kwambiri nthaka nʼkuchititsa kuti mbewu zimere ndi kubereka zipatso,Nʼkupereka mbewu kuti anthu adzale komanso chakudya kuti adye, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 55:10 Nsanja ya Olonda,9/1/2008, tsa. 27 Galamukani!,12/2008, ptsa. 6-7 Yesaya 2, ptsa. 244-246