Yesaya 56:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Wosangalala ndi munthu amene amachita zimenezi,Ndiponso mwana wa munthu amene amatsatira zimenezi,Amene amasunga Sabata ndipo salidetsa+Komanso amaletsa dzanja lake kuti lisachite choipa chilichonse. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:2 Yesaya 2, ptsa. 248-249
2 Wosangalala ndi munthu amene amachita zimenezi,Ndiponso mwana wa munthu amene amatsatira zimenezi,Amene amasunga Sabata ndipo salidetsa+Komanso amaletsa dzanja lake kuti lisachite choipa chilichonse.