Yesaya 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mlendo amene wayamba kulambira Yehova+ asanene kuti,‘Ndithu Yehova adzandilekanitsa ndi anthu ake.’ Ndipo munthu wofulidwa asanene kuti, ‘Inetu ndine mtengo wouma.’” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 56:3 Yesaya 2, ptsa. 249-252
3 Mlendo amene wayamba kulambira Yehova+ asanene kuti,‘Ndithu Yehova adzandilekanitsa ndi anthu ake.’ Ndipo munthu wofulidwa asanene kuti, ‘Inetu ndine mtengo wouma.’”