-
Yesaya 56:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Izi nʼzimene Yehova wanena kwa anthu ofulidwa amene amasunga sabata langa. Amene asankha kuchita zimene ndimasangalala nazo komanso amene amatsatira pangano langa:
-