Yesaya 58:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chifukwa cha inu, anthu adzamanganso mabwinja akalekale,+Ndipo mudzabwezeretsa maziko a mibadwo yakale.+ Mudzatchedwa womanga makoma ogumuka,+Ndiponso wokonza misewu kuti anthu azikhala mʼmphepete mwake. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:12 Yesaya 2, tsa. 285
12 Chifukwa cha inu, anthu adzamanganso mabwinja akalekale,+Ndipo mudzabwezeretsa maziko a mibadwo yakale.+ Mudzatchedwa womanga makoma ogumuka,+Ndiponso wokonza misewu kuti anthu azikhala mʼmphepete mwake.