Yesaya 58:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukatero mudzasangalala kwambiri mwa Yehova,Ndipo ine ndidzakuchititsani kuti mukwere mʼmalo apamwamba a dziko lapansi.+ Ndidzakuchititsani kuti mudye* zochokera mʼcholowa cha Yakobo kholo lanu,+Chifukwa pakamwa pa Yehova panena.” Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 58:14 Yesaya 2, ptsa. 285-287, 288-289
14 Mukatero mudzasangalala kwambiri mwa Yehova,Ndipo ine ndidzakuchititsani kuti mukwere mʼmalo apamwamba a dziko lapansi.+ Ndidzakuchititsani kuti mudye* zochokera mʼcholowa cha Yakobo kholo lanu,+Chifukwa pakamwa pa Yehova panena.”