Yesaya 59:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Palibe amene amafuula poikira kumbuyo chilungamo,+Ndipo palibe amene amalankhula zoona akapita kukhoti. Iwo amakhulupirira zinthu zachabechabe+ ndipo amalankhula zopanda pake. Iwo atenga pakati pa mavuto ndipo abereka zopweteka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 59:4 Yesaya 2, ptsa. 291-292
4 Palibe amene amafuula poikira kumbuyo chilungamo,+Ndipo palibe amene amalankhula zoona akapita kukhoti. Iwo amakhulupirira zinthu zachabechabe+ ndipo amalankhula zopanda pake. Iwo atenga pakati pa mavuto ndipo abereka zopweteka.+