Yesaya 61:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo adzamanganso malo amene akhala bwinja kwa nthawi yaitali.Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale,+Adzakonzanso mizinda imene inawonongedwa,+Malo amene akhala ali osakazidwa kumibadwomibadwo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:4 Yesaya 2, tsa. 327
4 Iwo adzamanganso malo amene akhala bwinja kwa nthawi yaitali.Adzamanga malo amene anasakazidwa kalekale,+Adzakonzanso mizinda imene inawonongedwa,+Malo amene akhala ali osakazidwa kumibadwomibadwo.+