Yesaya 61:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mʼmalo mwa manyazi, mudzalandira madalitso ochuluka kuwirikiza kawiri,Ndipo mʼmalo mochita manyazi, mudzafuula mosangalala chifukwa cha gawo lanu. Inde, mudzalandira madalitso owirikiza kawiri mʼdziko lanu,+ Ndipo mudzasangalala mpaka kalekale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:7 Yesaya 2, tsa. 330
7 Mʼmalo mwa manyazi, mudzalandira madalitso ochuluka kuwirikiza kawiri,Ndipo mʼmalo mochita manyazi, mudzafuula mosangalala chifukwa cha gawo lanu. Inde, mudzalandira madalitso owirikiza kawiri mʼdziko lanu,+ Ndipo mudzasangalala mpaka kalekale.+