Yesaya 61:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chifukwa ine Yehova ndimakonda chilungamo.+Ndimadana ndi zauchifwamba komanso zinthu zopanda chilungamo.+ Anthu anga ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,Ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 11 Yesaya 2, tsa. 332
8 Chifukwa ine Yehova ndimakonda chilungamo.+Ndimadana ndi zauchifwamba komanso zinthu zopanda chilungamo.+ Anthu anga ndidzawapatsa malipiro awo mokhulupirika,Ndipo ndidzachita nawo pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale.+