Yesaya 61:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 61:9 Nsanja ya Olonda,1/15/2007, tsa. 11 Yesaya 2, ptsa. 332-333
9 Ana awo* adzadziwika pakati pa mitundu ya anthu,+Ndipo mbadwa zawo zidzadziwika pakati pa anthu osiyanasiyana. Anthu onse owaona adzawazindikira,Kuti ndi ana amene* Yehova anawadalitsa.”+