-
Yesaya 62:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Iwe Yerusalemu, ine ndaika alonda pamakoma a mpanda wako.
Nthawi zonse, masana onse komanso usiku wonse, iwo asakhale chete.
Inu amene mukutchula dzina la Yehova,
Musapumule,
-