Yesaya 63:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amene anawachititsa kuti adutse pamadzi amphamvu*Moti anayenda osapunthwa,Mofanana ndi hatchi mʼchipululu?*
13 Amene anawachititsa kuti adutse pamadzi amphamvu*Moti anayenda osapunthwa,Mofanana ndi hatchi mʼchipululu?*