Yesaya 63:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nʼchifukwa chiyani inu Yehova mukuchititsa kuti tichoke panjira zanu? Nʼchifukwa chiyani mukuumitsa mtima wathu kuti tisakuopeni?+ Bwererani chifukwa cha atumiki anu,Mafuko omwe ndi cholowa chanu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 63:17 Yesaya 2, ptsa. 361-363
17 Nʼchifukwa chiyani inu Yehova mukuchititsa kuti tichoke panjira zanu? Nʼchifukwa chiyani mukuumitsa mtima wathu kuti tisakuopeni?+ Bwererani chifukwa cha atumiki anu,Mafuko omwe ndi cholowa chanu.+