-
Yesaya 64:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Ngati mmene zimakhalira moto ukayatsa tchire la zitsamba,
Ndiponso ukachititsa kuti madzi awire.
Zikanatero adani anu akanadziwa dzina lanu,
Ndipo mitundu ya anthu ikanachita mantha pamaso panu.
-