Yesaya 64:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Poona zinthu zonsezi, kodi mupitiriza kumangokhala osachitapo kanthu, inu Yehova? Kodi mungokhala chete nʼkumaonerera ife tikusautsidwa koopsa?+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 64:12 Yesaya 2, ptsa. 369-370
12 Poona zinthu zonsezi, kodi mupitiriza kumangokhala osachitapo kanthu, inu Yehova? Kodi mungokhala chete nʼkumaonerera ife tikusautsidwa koopsa?+