Yesaya 66:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mkazi anabereka asanayambe kumva zowawa za pobereka.+ Asanayambe kumva ululu wa pobereka, iye anabereka mwana wamwamuna. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 66:7 Yesaya 2, ptsa. 397-398 Nsanja ya Olonda,1/1/1995, tsa. 11
7 Mkazi anabereka asanayambe kumva zowawa za pobereka.+ Asanayambe kumva ululu wa pobereka, iye anabereka mwana wamwamuna.