-
Yesaya 66:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 “Kodi ine ndingachititse kuti mwana atsale pangʼono kubadwa koma nʼkumulepheretsa kuti abadwe?” akutero Yehova.
“Kapena kodi ndingachititse kuti mwana ayambe kubadwa kenako nʼkutseka chiberekero?” akutero Mulungu wanu.
-