-
Yesaya 66:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 “Popeza ndikudziwa ntchito zawo ndi maganizo awo, ine ndikubwera kudzasonkhanitsa pamodzi anthu a mitundu yonse ndi zilankhulo zonse ndipo iwo adzabwera nʼkuona ulemerero wanga.
-