Yeremiya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Yehova anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani Yeremiya?” Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona nthambi ya mtengo wa amondi.”* Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, ptsa. 8-9 Galamukani!,9/8/1987, tsa. 27
11 Ndiyeno Yehova anandifunsa kuti: “Ukuona chiyani Yeremiya?” Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona nthambi ya mtengo wa amondi.”*