Yeremiya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anandifunsanso kachiwiri kuti: “Ukuona chiyani?” Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mphika wa kukamwa kwakukulu umene ukuwira* ndipo wafulatira kumpoto koma kukamwa kwake kwaloza kumʼmwera.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:13 Yeremiya, ptsa. 14-15
13 Yehova anandifunsanso kachiwiri kuti: “Ukuona chiyani?” Ine ndinayankha kuti: “Ndikuona mphika wa kukamwa kwakukulu umene ukuwira* ndipo wafulatira kumpoto koma kukamwa kwake kwaloza kumʼmwera.”