Yeremiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako ndinakulowetsani mʼdziko la minda ya zipatso,Kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino zamʼdzikolo.+ Koma inu munalowa mʼdziko langa nʼkuliipitsa.Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+
7 Kenako ndinakulowetsani mʼdziko la minda ya zipatso,Kuti mudye zipatso zake ndi zinthu zabwino zamʼdzikolo.+ Koma inu munalowa mʼdziko langa nʼkuliipitsa.Cholowa changa munachisandutsa chinthu chonyansa.+