Yeremiya 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘Ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,Zolakwa zako ndidzazionabe ngati zinthu zothimbirira,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
22 ‘Ngakhale utasambira soda ndiponso sopo wambiri,Zolakwa zako ndidzazionabe ngati zinthu zothimbirira,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.