-
Yeremiya 2:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Unganene bwanji kuti, ‘Sindinadziipitse.
Sindinatsatire mafano a Baalaʼ?
Ganizira bwinobwino mmene ukuyendera mʼchigwa.
Ganizira zimene wachita.
Uli ngati ngamila yaingʼono yaikazi yothamanga kwambiri,
Imene ikuthamanga kupita uku ndi uku popanda cholinga,
-