Yeremiya 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mkazi iwe wachita zinthu mwaluso pofunafuna amuna oti akukonde. Wadziphunzitsa kuchita zinthu zoipa.+
33 Mkazi iwe wachita zinthu mwaluso pofunafuna amuna oti akukonde. Wadziphunzitsa kuchita zinthu zoipa.+