Yeremiya 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pamwamba pa mapiri pamveka phokoso,La kulira ndi kuchonderera kwa Aisiraeli,Chifukwa akhotetsa njira zawoNdipo aiwala Yehova Mulungu wawo.+
21 Pamwamba pa mapiri pamveka phokoso,La kulira ndi kuchonderera kwa Aisiraeli,Chifukwa akhotetsa njira zawoNdipo aiwala Yehova Mulungu wawo.+