Yeremiya 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsuka mtima wako nʼkuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi udzakhala ndi maganizo oipa mpaka liti?
14 Tsuka mtima wako nʼkuchotsa zoipa zonse, iwe Yerusalemu, kuti upulumuke.+ Kodi udzakhala ndi maganizo oipa mpaka liti?