Yeremiya 4:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina.Lengezani kuti zimenezi zidzachitikira Yerusalemu.” “Akazitape* akubwera kuchokera kudziko lakutaliNdipo adzalengeza mofuula zimene zidzachitikire mizinda ya Yuda.
16 Nenani zimenezi kwa anthu a mitundu ina.Lengezani kuti zimenezi zidzachitikira Yerusalemu.” “Akazitape* akubwera kuchokera kudziko lakutaliNdipo adzalengeza mofuula zimene zidzachitikire mizinda ya Yuda.