Yeremiya 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndikumva uthenga wa masoka otsatizanatsatizana,Chifukwa dziko lonse lawonongedwa. Mwadzidzidzi matenti anga awonongedwaMʼkanthawi kochepa nsalu za matenti anga zawonongedwa.+
20 Ndikumva uthenga wa masoka otsatizanatsatizana,Chifukwa dziko lonse lawonongedwa. Mwadzidzidzi matenti anga awonongedwaMʼkanthawi kochepa nsalu za matenti anga zawonongedwa.+